当前位置:首页 >> The Very Best >> Hear Me

LRC歌词

[04:40.00]CHICHEWA
[04:40.00]Siyani dumbo
[04:40.00]Siyani umbombo
[04:40.00]Tatopa nazo kodi simukudziwa kuti lija ndi kale?
[04:40.00]Siya umbanda
[04:40.00]Siya zauchigawenga
[04:40.00]Kodi watani iwe siukudziwa kuti kupha ndi sambi?
[04:40.00]Siyani dumbo
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Siya kaduka
[04:40.00]Siya zokonda kuba
[04:40.00]Siyani chinyengo kuyambila lero tiyeni tikonze tsogolo
[04:40.00]Siyani kugona
[04:40.00]Siya kugona tulo
[04:40.00]Kunja kwacha kodi simukuona kuti dzuwa latuluka?
[04:40.00]Siya kaduka
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Hear me now
[04:40.00]Dzaka makumi asanu
[04:40.00]Zatha kufika lero
[04:40.00]Mpaka lero umphawi
[04:40.00]Ukungophabe dziko
[04:40.00]Dzaka makumi asanu
[04:40.00]Zatha kufika lero
[04:40.00]Mpaka lero umphawi
[04:40.00]Ukungophabe dziko

文本歌词

CHICHEWA
Siyani dumbo
Siyani umbombo
Tatopa nazo kodi simukudziwa kuti lija ndi kale?
Siya umbanda
Siya zauchigawenga
Kodi watani iwe siukudziwa kuti kupha ndi sambi?
Siyani dumbo
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Siya kaduka
Siya zokonda kuba
Siyani chinyengo kuyambila lero tiyeni tikonze tsogolo
Siyani kugona
Siya kugona tulo
Kunja kwacha kodi simukuona kuti dzuwa latuluka?
Siya kaduka
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Dzaka makumi asanu
Zatha kufika lero
Mpaka lero umphawi
Ukungophabe dziko
Dzaka makumi asanu
Zatha kufika lero
Mpaka lero umphawi
Ukungophabe dziko
  • LRC下载
  • JSON下载
  • 文本下载
  • 推荐音乐

    更多

    推荐视频

    更多